A bungwe a abambo, Catholic Men Association, akupanga msonkhano wawo waukulu (Annual General Meeting) ku Parish ya St Martin de Porres, Dedza. Mutu wamsonkhanowu nd Bambo wa Chikatolika wodzetsa Chiyembekezo M’banja, mu Mpingo komanso M’dziko.

catholic men association dedza diocese agm

Msonkhanowu wayamba Lachisanu pa 26 September 2025 ndi Nsembe ya Misa yomwe anatsogolera ndi a Vicar General, Bambo John Chithonje.

Abambo okwana 200 ndi amene afika ku msonkhanowu.

catholic men association dedza diocese agm